close
Jump to content

Chingerezi

Kuchokera ku Wikipedia
Image

Ndiponso English ina imalankhulidwa ku dziko la America.Galamala yake imafanana koma mawu ena amasiyana.wachitsanzo ena amati hey dziko lina amati hello. English, pa Chichewa amati Chingerezi, ndi chilankhulo cha azungu ochokela ku Britain.